Mateyu 15:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Iye sanamyankha mau amodzi. Ndipo ophunzira ace anadza, nampempha, nati, Mumuuze amuke; pakuti apfuula pambuyo pathu.

Mateyu 15

Mateyu 15:20-27