Mateyu 14:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Iye anawauza makamuwo, anakwera m'phiri pa yekha, kukapemphera: ndipo pamene panali madzulo, Iye anakhala kumeneko yekha.

Mateyu 14

Mateyu 14:21-27