Mateyu 13:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 3 pofika ku dziko la kwao, anaphunzitsa iwo m'sunagoge mwao, kotero kuti anazizwa, nanena, Uyu adazitengakuti nzeru zimenezi ndi zamphamvu izi?

Mateyu 13

Mateyu 13:52-58