Mateyu 13:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ufumu wa Kumwamba uli wofanana ndi cuma cobisika m'munda; cimene munthu anacipeza, nacibisa; ndipo m'kucikonda kwace acoka, nagulitsa zonse ali nazo, nagula munda umenewu.

Mateyu 13

Mateyu 13:38-53