Mateyu 13:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwana wa munthu adzatuma angelo ace, ndipo iwo adzasonkhanitsa pamodzi, ndi kucotsa mu Ufumu wace zokhumudwitsa zonse, ndi anthu akucita kusayeruzika,

Mateyu 13

Mateyu 13:40-47