Mateyu 13:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anyamata ace a mwini nyumbayo anadza, nati kwa iye, Mbuye, kodi simunafesa mbeu zabwino m'munda mwanu? nanga wacokera kuti namsongoleyo?

Mateyu 13

Mateyu 13:22-33