Mateyu 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo makamu ambiri a anthu anasonkhanira kwa Iye, kotero kuti Iye analowa m'ngalawa, nakhala pansi, ndipo khamu lonse linaima pamtunda.

Mateyu 13

Mateyu 13:1-12