Mateyu 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu ali yense wakumva mau a Ufumu, osawadziwitsai, woipayo angodza, nakwatula cofesedwaco mumtima mwace. Uyo ndiye wofesedwa m'mbali mwa njira.

Mateyu 13

Mateyu 13:11-29