Mateyu 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anayankha nati, Cifukwa kwapatsidwa kwa inu kudziwa zinsinsi za Ufumu wa Kumwamba, koma sikunapatsidwa kwa iwo.

Mateyu 13

Mateyu 13:6-20