Mateyu 12:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti 6 ali yense amene adzacita cifuniro ca Atate wanga wa Kumwamba, yemweyo ndiye mbale wanga, ndi mlongo wanga, ndi amai wanga.

Mateyu 12

Mateyu 12:49-50