Mateyu 12:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo unena, ndidzabwerera kunka kunyumba kwanga, konkuja ndinaturukako; ndipo pakufikako uipeza yopanda wokhalamo, yosesedwa ndi yokonzedwa.

Mateyu 12

Mateyu 12:38-50