Mateyu 12:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti monga Yona anali m'mimba mwa cinsomba masiku atatu ndi usiku wace, comweco Mwana wa munthu adzakhala mumtima mwa dziko lapansi masiku atatu ndi usiku wace.

Mateyu 12

Mateyu 12:31-48