Mateyu 12:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinena kwa inu, kuti mau onse opanda pace, amene anthu adzalankhula, adzawawerengera mlandu wace tsiku la kuweruza.

Mateyu 12

Mateyu 12:31-41