Mateyu 12:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kapena akhoza bwanji munthu kulowa m'banja la munthu wolimba, ndi kufunkha akatundu ace, ngati iye sayamba kumanga munthu wolimbayo? ndipo pamenepo adzafunkha za m'banja lace.

Mateyu 12

Mateyu 12:26-33