Mateyu 12:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu anadziwa maganizo ao, nati kwa iwo, Ufumu uti wonse wogawanika pa wokha sukhalira kupasuka, ndi mudzi uti wonse kapena banja logawanika pa lokha silidzakhala;

Mateyu 12

Mateyu 12:18-34