Mateyu 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo anabwera naye kwa Iye munthu wogwidwa ndi ciwanda, wakhungu ndi wosalankhula; ndipo Iye anamciritsa, kotero kuti wosalankhulayo analankhula, napenya.

Mateyu 12

Mateyu 12:13-29