Mateyu 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu m'mene anadziwa, anacokera kumeneko: ndipo anamtsata Iye anthu ambiri; ndipo Iye anawaciritsa iwo onse,

Mateyu 12

Mateyu 12:6-21