Mateyu 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo onani, munali munthu wa dzanja lopuwala, Ndipo anamfunsitsa Iye, ndi kuti, Nkuloleka kodi kuciritsa tsiku la Sabata? kuti ampalamulitse mlandu.

Mateyu 12

Mateyu 12:2-17