Mateyu 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyengo imeneyo Yesu anapita tsiku la Sabata pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace anali ndi njala, nayamba kubudula ngala, nadya.

Mateyu 12

Mateyu 12:1-5