Mateyu 11:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene iwo analikumuka, Yesu anayambonena Ndi makamu a anthu za kwa Yohane, Munaturuka kunka kucipululu kukapenyanji? Bango logwedezeka nd: mphepo kodi?

Mateyu 11

Mateyu 11:1-13