Mateyu 11:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akhungu alandira kuona kwao, Ndi opunduka miyendo ayenda, akhate akonzedwa, indi ogontha akumva, ndi akufa aukitsidwa, ndi kwa aumphawi ulalikidwa uthenga wabwino.

Mateyu 11

Mateyu 11:1-14