Mateyu 11:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zinthu zonse zinaperekedwa kwa Ine ndi Atate wanga; ndipo palibe munthu adziwa Mwana, koma Atate yekha; ndi palibe wina adziwa Atate, koma M wana yekha, ndi iye amene Mwana afuna kumuululira.

Mateyu 11

Mateyu 11:17-30