Mateyu 11:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyengo imeneyo Yesu anayankha nati, Ndibvomerezana ndi Inu, Atate, Mwini Kumwamba ndi dziko lapansi, kuti munazibisira izo kwa anzeru ndi akudziwitsa, ndipo munaziululira zomwe kwa makanda:

Mateyu 11

Mateyu 11:22-30