Mateyu 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwana wa munthu anadza wakudya, ndi wakumwa, ndipo iwo amati, Onani munthu wakudyaidya ndi wakumwaimwa vinyo, bwenzi la amisonkho ndi ocimwa! Ndipo nzeru iyesedwa yolungama ndi nchito zace.

Mateyu 11

Mateyu 11:16-20