Mateyu 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, pamene Yesu anatha kuwafotokozera ophunzira ace khumi Ndi awiri, Iye anacokera kumeneko kukaphunzitsa Ndi kulalikira m'midzi mwao.

Mateyu 11

Mateyu 11:1-6