Mateyu 10:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa amene, khumi ndi awiriwa, Yesu anawatumiza, nawalangiza ndi kuti,Musapite ku njira ya kwa anthu akunja, ndi m'mudzi wa Asamariya musamalowamo:

Mateyu 10

Mateyu 10:1-11