Mateyu 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kumkwanira wophunzira kuti akhale monga mphunzitsi wace, ndi kapolo monga mbuye. Ngati anamucha mwini banja Beelzebule, sadzaposa kodi kuwatero apabanja ace?

Mateyu 10

Mateyu 10:21-33