Mateyu 1:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo Yosefe anauka tulo tace, nacita monga anamuuza mngelo wa Ambuye, nadzitengera yekha mkazi wace;

25. ndipo sanamdziwa iye kufikira atabala rriwana wace; namucha dzina lace Yesu.

Mateyu 1