Masalmo 99:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munawayankha, Yehova Mulungu wathu:Munawakhalira Mulungu wakuwakhululukira,Mungakhale munabwezera cilango pa zocita zao.

Masalmo 99

Masalmo 99:3-9