Masalmo 97:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Inu, Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi,Ndinu wokwezeka kwakukuru pamwamba pa milungu yonse yina.

Masalmo 97

Masalmo 97:1-12