Masalmo 93:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu;Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'cuuno;Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka.

Masalmo 93

Masalmo 93:1-5