Masalmo 90:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Asanabadwe mapiri,Kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu,Inde, kuyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha,Inu ndinu Mulungu.

Masalmo 90

Masalmo 90:1-7