Masalmo 9:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Ukani, Yehova, asalimbike munthu;Amitundu aweruzidwe pankhope panu.

20. Muwacititse mantha, Yehova; Adziwe amitundu kuti ali anthu.

Masalmo 9