Masalmo 86:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Sungani moyo wanga pakuti ine ndine wokondedwa wanu;Inu Mulungu wanga, pulumutsani mtumiki wanu wokhulupirira Inu.

3. Mundicitire cifundo, Ambuye;Pakuti tsiku lonse ndiitana Inu.

4. Kondwetsani moyo wa mtumiki wanu;Pakuti ndikwezera moyo wanga kwa Inu, Ambuye.

Masalmo 86