Masalmo 85:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Inde Yehova adzapereka zokoma;Ndipo dziko lathu lidzapereka zipatso zace.

13. Cilungamo cidzamtsogolera; Nicidzamkonzera mapazi ace njira.

Masalmo 85