Masalmo 84:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti tsiku limodzi m'mabwalo anu likoma koposa masiku ambirimbiri akukhala pena,Kukhala inewapakhomo m'nyumba ya Mulungu wanga,Kundikonda ine koposa kugonera m'mahema a coipa,

Masalmo 84

Masalmo 84:1-12