Masalmo 83:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Acititseni manyazi pankhope pao;Kuti afune dzina lanu, Yehova.

17. Acite manyazi, naopsedwe kosatha;Ndipo asokonezeke, naonongeke:

18. Kuti adziwe kuti inu nokha, dzina lanu ndinu Yehova,Ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi.

Masalmo 83