Masalmo 79:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapereka mitembo ya atumiki anu ikhale cakudya ca mbalame za mlengalenga,Nyama ya okondedwa anu anaipereka kwa zirombo za m'dziko.

Masalmo 79

Masalmo 79:1-6