Masalmo 75:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo;Ndinacirika mizati yace.

4. Ndinati kwa odzitamandira, Musamacita zodzitamandira;Ndi kwa oipa, Musamakweza nyanga;

5. Musamakwezetsa nyanga yanu;Musamalankhula ndi khosi louma.

6. Pakuti kukuzaku sikucokera kum'mawa,Kapena kumadzulo, kapena kucipululu,

Masalmo 75