Masalmo 72:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzina lace lidzakhala kosatha:Momwe likhalira dzuwa dzina lace lidzamvekera zidzukulu:Ndipo anthu adzadalitsidwa mwa Iye;Amitundu onse adzamucha wodala.

Masalmo 72

Masalmo 72:12-20