Masalmo 72:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu,Ndi mwana wa mfumu cilungamo canu.

2. Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m'cilungamo,Ndi ozunzika anu ndi m'ciweruzo.

3. Mapiri adzatengera anthu mtendere,Timapiri tomwe, m'cilungamo.

Masalmo 72