Masalmo 69:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo akuyembekeza Inu, Ambuve Yehova wa makamu, asacite manyazi cifukwa ca ine:Iwo ofuna Inu, Mulungu wa Israyeli, asapepulidwe cifukwa ca ine.

Masalmo 69

Masalmo 69:5-11