Masalmo 68:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basana,Ndidzawatenganso kozama kwa nyanja:

23. Kuti ubviike phazi lako m'mwazi,Kuti malilime a agaru ako alaweko adani ako.

24. Anapenya mayendedwe anu, Mulungu,Mayendedwe a Mulungu wanga, Mfumu yanga, m'malo oyera.

Masalmo 68