Masalmo 6:9-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Wamva Yehova kupemba kwanga;Yehova adzalandira pemphero langa.

10. Adzacita manyazi, nadzanthunthumira kwakukuru adani anga onse;Adzabwerera, nadzacita manyazi modzidzimuka,

Masalmo 6