Masalmo 58:10-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera cilango:Adzasamba mapazi ace m'mwazi wa woipa.

11. Ndipo anthu adzati, Indedi, pali mphotho kwa wolungama;Indedi, pali Mulungu wakuweruza pa dziko lapansi.

Masalmo 58