Masalmo 57:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima;Ndidzayimba, inde, ndidzayimba zolemekeza.

Masalmo 57

Masalmo 57:5-8