Masalmo 55:2-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Mveram, ndipo mundiyankhe:Ndiliralira m'kudandaula kwanga ndi kubuula;

3. Cifukwa ca mau a mdani,Cifukwa ca kundipsinja woipa;Pakuti andisenza zopanda pace,Ndipo adana nane mumkwiyo.

4. Mtima wanga uwawa m'kati mwanga;Ndipo zoopsa za imfa zandigwera.

Masalmo 55