Masalmo 53:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anaopa kwakukuru, popanda cifukwa ca kuopa:Pakuti Mulungu anamwaza mafupa a iwo akuzinga iwe;Unawacititsa manyazi, pakuti Mulungu anawakaniza.

Masalmo 53

Masalmo 53:1-6