Masalmo 50:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mulungu wa milungu, Yehova, wanena,Aitana dziko lapansi kuyambira kuturuka kwa dzuwa kufikira kulowa kwace.