Masalmo 5:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika;M'kati mwao m'mosakaza;M'mero mwao ndi manda apululu:Lilime lao asyasyalika nalo.

Masalmo 5

Masalmo 5:8-12